Genesis 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mwanayo anakula n’kumusiyitsa kuyamwa.+ Pa tsiku limene anamusiyitsa kuyamwalo, Abulahamu anakonza phwando lalikulu.
8 Tsopano mwanayo anakula n’kumusiyitsa kuyamwa.+ Pa tsiku limene anamusiyitsa kuyamwalo, Abulahamu anakonza phwando lalikulu.