Genesis 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero Sara anayamba kuuza Abulahamu kuti: “Thamangitsani kapolo wamkaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, chifukwa mwana wa kapolo ameneyu sadzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wanga Isaki.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:10 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 21
10 Chotero Sara anayamba kuuza Abulahamu kuti: “Thamangitsani kapolo wamkaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, chifukwa mwana wa kapolo ameneyu sadzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wanga Isaki.”+