Genesis 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Abimeleki anayankha kuti: “Sindikudziwa amene anachita zimenezi, ndipo ngakhale iwe sunandiuze. Inetu sindinamve za nkhani imeneyi, moti ndikuimvera pompano.”+
26 Abimeleki anayankha kuti: “Sindikudziwa amene anachita zimenezi, ndipo ngakhale iwe sunandiuze. Inetu sindinamve za nkhani imeneyi, moti ndikuimvera pompano.”+