Genesis 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho iwo anachita panganolo+ pa Beere-sebapo, kenako Abimeleki limodzi ndi Fikolo mkulu wa asilikali ake, anabwerera kudziko la Afilisiti.+
32 Choncho iwo anachita panganolo+ pa Beere-sebapo, kenako Abimeleki limodzi ndi Fikolo mkulu wa asilikali ake, anabwerera kudziko la Afilisiti.+