Genesis 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa izi, Adamu anatcha mkazi wake dzina lakuti Hava,*+ chifukwa anali kudzakhala mayi wa munthu aliyense wamoyo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:20 Nsanja ya Olonda,4/15/1999, tsa. 17
20 Pambuyo pa izi, Adamu anatcha mkazi wake dzina lakuti Hava,*+ chifukwa anali kudzakhala mayi wa munthu aliyense wamoyo.+