Genesis 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Patapita nthawi, Yakobo anamva zimene ana aamuna a Labani anali kunena, kuti: “Yakobo watenga chilichonse cha bambo athu, ndipo chuma chonse chimene wasonkhanitsachi chachokera kwa bambo athu.”+
31 Patapita nthawi, Yakobo anamva zimene ana aamuna a Labani anali kunena, kuti: “Yakobo watenga chilichonse cha bambo athu, ndipo chuma chonse chimene wasonkhanitsachi chachokera kwa bambo athu.”+