Genesis 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anapitiriza kuti, ‘Kweza maso ako ndipo ona kuti mbuzi zonse zamphongo zimene zikukwerazi ndi zamizeremizere, zamawangamawanga ndiponso zamathothomathotho. Ndachita zimenezi chifukwa ndaona zonse zimene Labani akuchita kwa iwe.+
12 Iye anapitiriza kuti, ‘Kweza maso ako ndipo ona kuti mbuzi zonse zamphongo zimene zikukwerazi ndi zamizeremizere, zamawangamawanga ndiponso zamathothomathotho. Ndachita zimenezi chifukwa ndaona zonse zimene Labani akuchita kwa iwe.+