Genesis 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ uja, kumene unadzoza mwala+ kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+
13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ uja, kumene unadzoza mwala+ kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+