Genesis 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atamva zimenezo, iye anatenga abale ake n’kuyamba kuthamangira+ Yakobo. Iwo anayenda ulendo wa masiku 7, ndipo anamupeza m’dera la kumapiri la Giliyadi.
23 Atamva zimenezo, iye anatenga abale ake n’kuyamba kuthamangira+ Yakobo. Iwo anayenda ulendo wa masiku 7, ndipo anamupeza m’dera la kumapiri la Giliyadi.