-
Genesis 31:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kenako Labani anapita kwa Yakobo. Pa nthawiyi n’kuti Yakobo atamanga hema wake m’dera la kumapiri la Giliyadi, ndipo Labani ndi abale ake anamanganso hema wawo m’dera lomwelo.
-