-
Genesis 31:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Rakele anali atatenga aterafi aja n’kuwabisa m’chishalo choika pangamila, n’kuchikhalira. Labani anafunafuna muhema monsemo, koma sanawapeze aterafiwo.
-