Genesis 31:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Nyama yanu iliyonse imene inakhadzulidwa ndi chilombo sindinaibweretse kwa inu.+ Ndinali kuitenga kukhala yanga. Kaya ina ibedwe usana kapena usiku, munali kundiuza kuti ndikulipireni.+
39 Nyama yanu iliyonse imene inakhadzulidwa ndi chilombo sindinaibweretse kwa inu.+ Ndinali kuitenga kukhala yanga. Kaya ina ibedwe usana kapena usiku, munali kundiuza kuti ndikulipireni.+