Genesis 31:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zonse pamodzi ndakhala zaka 20 m’nyumba mwanu. Ndakugwirirani ntchito zaka 14, kugwirira ana anu aakazi awiriwa. Zaka zinanso 6, ndagwirira ntchito ziweto. Koma inu munapitiriza kusinthasintha malipiro anga mpaka maulendo 10.+
41 Zonse pamodzi ndakhala zaka 20 m’nyumba mwanu. Ndakugwirirani ntchito zaka 14, kugwirira ana anu aakazi awiriwa. Zaka zinanso 6, ndagwirira ntchito ziweto. Koma inu munapitiriza kusinthasintha malipiro anga mpaka maulendo 10.+