Genesis 31:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Labani anapitiriza kulankhula kuti: “Mulu wa miyalawu ndi mboni yathu lero pakati pa ine ndi iwe.” N’chifukwa chake unatchedwa Galeeda,+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:48 Utumiki Komanso Moyo Wathu,4/2020, tsa. 4
48 Labani anapitiriza kulankhula kuti: “Mulu wa miyalawu ndi mboni yathu lero pakati pa ine ndi iwe.” N’chifukwa chake unatchedwa Galeeda,+