Genesis 31:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Ukamakazunza ana angawa,+ ndipo ukakatenga akazi ena kuwonjezera pa ana anga, ngakhale palibe munthu pano, dziwa kuti Mulungu ndiye mboni pakati pa ine ndi iwe.”+
50 Ukamakazunza ana angawa,+ ndipo ukakatenga akazi ena kuwonjezera pa ana anga, ngakhale palibe munthu pano, dziwa kuti Mulungu ndiye mboni pakati pa ine ndi iwe.”+