Genesis 31:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Muluwu ndiponso mwala wachikumbutsowu ndi mboni.+ Zikuchitira umboni kuti, pakati pa ine ndi iwe, wina sadzadutsa muluwu ndi mwala wachikumbutsowu kukachitira mnzake choipa.+
52 Muluwu ndiponso mwala wachikumbutsowu ndi mboni.+ Zikuchitira umboni kuti, pakati pa ine ndi iwe, wina sadzadutsa muluwu ndi mwala wachikumbutsowu kukachitira mnzake choipa.+