Genesis 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ndili ndi ng’ombe, abulu, nkhosa, komanso antchito aamuna ndi aakazi.+ Ndatumiza amithenga kwa mbuyanga kukupemphani kuti mundikomere mtima.”’”+
5 Tsopano ndili ndi ng’ombe, abulu, nkhosa, komanso antchito aamuna ndi aakazi.+ Ndatumiza amithenga kwa mbuyanga kukupemphani kuti mundikomere mtima.”’”+