Genesis 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amithengawo atabwerako, anauza Yakobo kuti: “Tinakafika kwa m’bale wanu Esau, ndipo iyenso ali m’njira kudzakumana nanu. Akubwera limodzi ndi amuna 400.”+
6 Amithengawo atabwerako, anauza Yakobo kuti: “Tinakafika kwa m’bale wanu Esau, ndipo iyenso ali m’njira kudzakumana nanu. Akubwera limodzi ndi amuna 400.”+