Genesis 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atamva zimenezi, Yakobo anachita mantha ndi kuda nkhawa kwambiri.+ Chotero anagawa anthu amene anali nawo m’magulu awiri, kuphatikizapo nkhosa, mbuzi, ng’ombe ndi ngamila.+
7 Atamva zimenezi, Yakobo anachita mantha ndi kuda nkhawa kwambiri.+ Chotero anagawa anthu amene anali nawo m’magulu awiri, kuphatikizapo nkhosa, mbuzi, ng’ombe ndi ngamila.+