Genesis 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anati: “Ngati Esau angafikire gulu limodzi kuti alithire nkhondo, gulu linalo lingathe kuthawa.”+
8 Kenako anati: “Ngati Esau angafikire gulu limodzi kuti alithire nkhondo, gulu linalo lingathe kuthawa.”+