Genesis 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsiku limeneli Yakobo anagona pamalopo. Kenako pa chuma chake anapatulapo zinthu zoti akapatse m’bale wake Esau ngati mphatso.+
13 Tsiku limeneli Yakobo anagona pamalopo. Kenako pa chuma chake anapatulapo zinthu zoti akapatse m’bale wake Esau ngati mphatso.+