Genesis 32:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero anapatsa anyamata ake magulu a ziwetozo, gulu lililonse palokha. Kenako anawalangiza mobwerezabwereza kuti: “Tsogolani muwoloke mtsinje, ndipo muzisiya mpata pakati pa gulu lililonse la ziweto.”+
16 Atatero anapatsa anyamata ake magulu a ziwetozo, gulu lililonse palokha. Kenako anawalangiza mobwerezabwereza kuti: “Tsogolani muwoloke mtsinje, ndipo muzisiya mpata pakati pa gulu lililonse la ziweto.”+