-
Genesis 32:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndiyeno analangiza mnyamata woyamba kuti: “Ngati angakumane nawe Esau m’bale wanga n’kukufunsa kuti, ‘Kodi mbuyako ndani? Ndipo ukupita kuti? Nanga ziweto zimene ukukusazi n’zandani?’
-