Genesis 32:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nayenso Yakobo anafunsa kuti: “Nawenso ndiuze dzina lako.” Koma iye anati: “Ukufunsiranji dzina langa?”+ Atatero, anamudalitsa pamalo amenewo.
29 Nayenso Yakobo anafunsa kuti: “Nawenso ndiuze dzina lako.” Koma iye anati: “Ukufunsiranji dzina langa?”+ Atatero, anamudalitsa pamalo amenewo.