Genesis 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Dina, mwana wamkazi amene Leya+ anaberekera Yakobo, ankakonda kukacheza+ ndi ana aakazi a m’dzikolo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:1 Nsanja ya Olonda,8/1/2001, tsa. 202/1/1997, tsa. 30
34 Dina, mwana wamkazi amene Leya+ anaberekera Yakobo, ankakonda kukacheza+ ndi ana aakazi a m’dzikolo.+