Genesis 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yakobo anamva zakuti Sekemu wagwiririra mwana wake Dina. Pa nthawiyo n’kuti ana ake aamuna ali kubusa ndi ziweto zake.+ Choncho, Yakobo sananene kanthu kudikira kuti ana akewo abwere.+
5 Tsopano Yakobo anamva zakuti Sekemu wagwiririra mwana wake Dina. Pa nthawiyo n’kuti ana ake aamuna ali kubusa ndi ziweto zake.+ Choncho, Yakobo sananene kanthu kudikira kuti ana akewo abwere.+