Genesis 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Hamori anawauza kuti: “Mwana wanga Sekemu wakonda mtsikana wanuyu ndi mtima wonse.+ Chonde, m’patseni kuti akhale mkazi wake.+
8 Ndiyeno Hamori anawauza kuti: “Mwana wanga Sekemu wakonda mtsikana wanuyu ndi mtima wonse.+ Chonde, m’patseni kuti akhale mkazi wake.+