Genesis 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ana a Yakobo anayankha Sekemu ndi bambo ake Hamori mowapita pansi. Anatero chifukwa Sekemu anali atagwiririra Dina mlongo wawo.+
13 Koma ana a Yakobo anayankha Sekemu ndi bambo ake Hamori mowapita pansi. Anatero chifukwa Sekemu anali atagwiririra Dina mlongo wawo.+