Genesis 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero mnyamatayu sanachedwe kuchita zimene anauzidwazo+ chifukwa anamukonda kwambiri mwana wa Yakobo. Sekemuyo anali wolemekezeka kwambiri+ m’nyumba yonse ya bambo ake.+
19 Chotero mnyamatayu sanachedwe kuchita zimene anauzidwazo+ chifukwa anamukonda kwambiri mwana wa Yakobo. Sekemuyo anali wolemekezeka kwambiri+ m’nyumba yonse ya bambo ake.+