Ekisodo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pamene Yakobo, kapena kuti Isiraeli anapita ku Iguputo, aliyense mwa ana ake aamuna anapitanso limodzi ndi banja lake. Mayina a ana a Yakobowo ndi awa:+
1 Pamene Yakobo, kapena kuti Isiraeli anapita ku Iguputo, aliyense mwa ana ake aamuna anapitanso limodzi ndi banja lake. Mayina a ana a Yakobowo ndi awa:+