Ekisodo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Patapita nthawi Yosefe anamwalira.+ Ndipo abale ake onse ndi m’badwo wonsewo anamwaliranso.