Ekisodo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pamene anali kuwazunza kwambiri m’pamenenso anali kuwonjezeka ndi kufalikira mowirikiza, mwakuti Aiguputo anachita mantha kwambiri ndi ana a Isiraeliwo.+
12 Koma pamene anali kuwazunza kwambiri m’pamenenso anali kuwonjezeka ndi kufalikira mowirikiza, mwakuti Aiguputo anachita mantha kwambiri ndi ana a Isiraeliwo.+