Ekisodo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho chifukwa chakuti azambawo anaopa Mulungu woona, m’kupita kwa nthawi iye anawadalitsa ndi mabanja awoawo.+
21 Choncho chifukwa chakuti azambawo anaopa Mulungu woona, m’kupita kwa nthawi iye anawadalitsa ndi mabanja awoawo.+