Ekisodo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anati: “Dzina lake akhale Gerisomu,*+ chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”+
22 Patapita nthawi Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anati: “Dzina lake akhale Gerisomu,*+ chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”+