Ekisodo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Mose anayankha Mulungu woona kuti: “Ndine ndani ine kuti ndipite kwa Farao ndi kutulutsa ana a Isiraeli ku Iguputo?”+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Nsanja ya Olonda,2/15/2005, ptsa. 13-14
11 Koma Mose anayankha Mulungu woona kuti: “Ndine ndani ine kuti ndipite kwa Farao ndi kutulutsa ana a Isiraeli ku Iguputo?”+