16 Pita, ukasonkhanitse akulu a Isiraeli ndi kuwauza kuti, ‘Yehova Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, anaonekera kwa ine+ n’kundiuza kuti: “Ndithu, ndidzakulanditsani ndi kuchitapo kanthu+ pa zonse zimene akukuchitirani mu Iguputo.