Ekisodo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Yehova anachita monga mmene Mose anapemphera,+ ndipo achule amene anali m’nyumba, m’mabwalo ndi m’minda anayamba kufa.
13 Pamenepo Yehova anachita monga mmene Mose anapemphera,+ ndipo achule amene anali m’nyumba, m’mabwalo ndi m’minda anayamba kufa.