27 pamenepo mudzawauze kuti, ‘Umenewu ndi mwambo wopereka nsembe ya pasika kwa Yehova,+ amene anapitirira nyumba za ana a Isiraeli mu Iguputo pamene anali kupha Aiguputo ndi mliri, koma anapulumutsa mabanja athu.’”
Atatero, anthu anagwada ndi kuweramira pansi.+