Ekisodo 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ponena za ana a Isiraeli, Farao adzati, ‘Asokonezeka ndipo akungoyendayenda m’dziko lathu. Chipululu chawatsekera.’+
3 Ndiyeno ponena za ana a Isiraeli, Farao adzati, ‘Asokonezeka ndipo akungoyendayenda m’dziko lathu. Chipululu chawatsekera.’+