Ekisodo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako mfumu ya Iguputo inauzidwa kuti Aisiraeli athawa. Pomwepo mtima wa Farao ndi atumiki ake unasinthanso ataganizira za Aisiraeli,+ moti anati: “Tachitanji pamenepa polola akapolo athu Aisiraeli kuchoka?”+
5 Kenako mfumu ya Iguputo inauzidwa kuti Aisiraeli athawa. Pomwepo mtima wa Farao ndi atumiki ake unasinthanso ataganizira za Aisiraeli,+ moti anati: “Tachitanji pamenepa polola akapolo athu Aisiraeli kuchoka?”+