Ekisodo 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho iwo anafunsa Mose kuti: “Kodi watibweretsa kuno kuti tidzafere m’chipululu muno chifukwa chakuti mu Iguputo mulibe manda?+ N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi, kutitulutsa mu Iguputo?
11 Choncho iwo anafunsa Mose kuti: “Kodi watibweretsa kuno kuti tidzafere m’chipululu muno chifukwa chakuti mu Iguputo mulibe manda?+ N’chifukwa chiyani watichitira zimenezi, kutitulutsa mu Iguputo?