Ekisodo 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi si zimene tinakuuza tili ku Iguputo, kuti, ‘Tisiye tizitumikira Aiguputo’? Chifukwa n’kwabwino kutumikira Aiguputo kusiyana n’kuti tifere m’chipululu.”+
12 Kodi si zimene tinakuuza tili ku Iguputo, kuti, ‘Tisiye tizitumikira Aiguputo’? Chifukwa n’kwabwino kutumikira Aiguputo kusiyana n’kuti tifere m’chipululu.”+