Ekisodo 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno mngelo+ wa Mulungu woona amene anali kuyenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka n’kupita kumbuyo kwawo. Motero, mtambo woima njo ngati chipilala uja unachoka kutsogolo n’kukaima kumbuyo kwawo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:19 Nsanja ya Olonda,2/1/1991, tsa. 17
19 Ndiyeno mngelo+ wa Mulungu woona amene anali kuyenda patsogolo pa Aisiraeli anachoka n’kupita kumbuyo kwawo. Motero, mtambo woima njo ngati chipilala uja unachoka kutsogolo n’kukaima kumbuyo kwawo.+