Ekisodo 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno pa nthawi ya ulonda wam’mawa,* Yehova ali mumtambo ndi moto woima njo ngati chipilala,+ anayang’ana gulu la Aiguputo, ndipo anachititsa Aiguputowo kusokonezeka.+
24 Ndiyeno pa nthawi ya ulonda wam’mawa,* Yehova ali mumtambo ndi moto woima njo ngati chipilala,+ anayang’ana gulu la Aiguputo, ndipo anachititsa Aiguputowo kusokonezeka.+