Ekisodo 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza panyanja,+ kuti madzi abwerere ndi kumiza Aiguputo, magaleta awo ankhondo ndi asilikali awo apamahatchi.”
26 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako ndi kuloza panyanja,+ kuti madzi abwerere ndi kumiza Aiguputo, magaleta awo ankhondo ndi asilikali awo apamahatchi.”