Ekisodo 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho madziwo anabwereradi,+ ndipo anamiza magaleta ankhondo ndi asilikali apamahatchi a magulu onse ankhondo a Farao, amene analondola Aisiraeli m’nyanjamo.+ Palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+
28 Choncho madziwo anabwereradi,+ ndipo anamiza magaleta ankhondo ndi asilikali apamahatchi a magulu onse ankhondo a Farao, amene analondola Aisiraeli m’nyanjamo.+ Palibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+