Ekisodo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+
30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+