Ekisodo 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo m’mawa mudzaona ulemerero wa Yehova+ chifukwa wamva kung’ung’udza kwanu kotsutsana ndi Yehovayo. Ife ndife ndani kuti muziting’ung’udzira?”
7 Ndipo m’mawa mudzaona ulemerero wa Yehova+ chifukwa wamva kung’ung’udza kwanu kotsutsana ndi Yehovayo. Ife ndife ndani kuti muziting’ung’udzira?”