Ekisodo 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova walamula kuti, ‘Tolani chakudya chimenecho, aliyense malinga ndi mmene amadyera.+ Muzitola malinga ndi chiwerengero cha anthu amene ali m’hema wanu. Munthu aliyense muzim’tolera muyezo wa omeri* limodzi.’”
16 Yehova walamula kuti, ‘Tolani chakudya chimenecho, aliyense malinga ndi mmene amadyera.+ Muzitola malinga ndi chiwerengero cha anthu amene ali m’hema wanu. Munthu aliyense muzim’tolera muyezo wa omeri* limodzi.’”