Ekisodo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akayeza chakudyacho pamuyezo wa omeri, munthu amene anatola chambiri sichinali kuposa muyezowo, ndipo amene anatola chochepa sichinali kuperewera.+ Aliyense anatola malinga ndi mmene amadyera.
18 Akayeza chakudyacho pamuyezo wa omeri, munthu amene anatola chambiri sichinali kuposa muyezowo, ndipo amene anatola chochepa sichinali kuperewera.+ Aliyense anatola malinga ndi mmene amadyera.